9 Koma ena anapitiriza kuchita makani komanso sankakhulupirira, ndipo ankanena zonyoza Njirayo+ pamaso pa anthu ambiri. Choncho iye anawachokera+ nʼkuchotsanso ophunzirawo pakati pawo. Ndipo tsiku ndi tsiku ankakamba nkhani muholo pasukulu ya Turano.