Machitidwe 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Ayuda ena amene ankayendayenda nʼkumatulutsa ziwanda, anayesa kutchula dzina la Ambuye Yesu pofuna kuchiritsa anthu amene anali ndi mizimu yoipa. Ankanena kuti: “Ndikukulamula mʼdzina la Yesu amene Paulo akumulalikira.”+
13 Koma Ayuda ena amene ankayendayenda nʼkumatulutsa ziwanda, anayesa kutchula dzina la Ambuye Yesu pofuna kuchiritsa anthu amene anali ndi mizimu yoipa. Ankanena kuti: “Ndikukulamula mʼdzina la Yesu amene Paulo akumulalikira.”+