-
Machitidwe 19:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako, munthu amene anali ndi mzimu woipa uja anawalumphira. Analimbana nawo mmodzimmodzi mpaka kuwagonjetsa onsewo, moti anatuluka mʼnyumbamo nʼkuthawa ali maliseche komanso atavulala.
-