-
Machitidwe 19:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Anthu onse anadziwa zimenezi, Ayuda ndi Agiriki amene ankakhala ku Efeso. Choncho onse anagwidwa ndi mantha ndipo dzina la Ambuye Yesu linapitiriza kulemekezedwa.
-