Machitidwe 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitachitika zimenezi, Paulo anatsimikiza mumtima mwake kupita ku Yerusalemu,+ kudzera ku Makedoniya+ ndi ku Akaya. Iye anati: “Ndikakafika kumeneko, ndikapitanso ku Roma.”+
21 Zitachitika zimenezi, Paulo anatsimikiza mumtima mwake kupita ku Yerusalemu,+ kudzera ku Makedoniya+ ndi ku Akaya. Iye anati: “Ndikakafika kumeneko, ndikapitanso ku Roma.”+