Machitidwe 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Panali munthu wina wosula siliva dzina lake Demetiriyo. Amisiri ankapindula kwambiri chifukwa cha ntchito yake yopanga tiakachisi tasiliva ta Atemi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:24 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 195/15/1990, tsa. 26
24 Panali munthu wina wosula siliva dzina lake Demetiriyo. Amisiri ankapindula kwambiri chifukwa cha ntchito yake yopanga tiakachisi tasiliva ta Atemi.+