-
Machitidwe 19:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudza zinthu zimenezi. Ndiyeno anawauza kuti: “Anthu inu, mukudziwa kuti timapeza chuma kuchokera mu ntchito imeneyi.
-