-
Machitidwe 19:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndipo chimene chikuopsa kwambiri si kunyozeka kwa ntchito yathu yokhayi, koma kachisi wa mulungu wamkulu wamkazi Atemi azidzaonedwa ngati wopanda pake. Mukudziwa kuti aliyense mʼchigawo chonse cha Asia komanso padziko lonse lapansi amalemekeza Atemi, koma chifukwa cha zimene Paulo akunena ulemerero wake udzatheratu.”
-