Machitidwe 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero mumzindawo munadzaza chisokonezo, ndipo anthu onse anathamangira mʼbwalo lamasewera, atagwira Gayo ndi Arisitako+ nʼkuwakokera mʼbwalomo. Gayo ndi Arisitako ankayenda ndi Paulo ndipo kwawo kunali ku Makedoniya. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:29 Nsanja ya Olonda,8/15/2007, tsa. 10
29 Zitatero mumzindawo munadzaza chisokonezo, ndipo anthu onse anathamangira mʼbwalo lamasewera, atagwira Gayo ndi Arisitako+ nʼkuwakokera mʼbwalomo. Gayo ndi Arisitako ankayenda ndi Paulo ndipo kwawo kunali ku Makedoniya.