-
Machitidwe 19:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Anthu ena oyangʼanira zikondwerero ndi masewera, amene anali anzake, nawonso anamutumizira uthenga womuchonderera kuti asaike moyo wake pachiswe pokalowa mʼbwalo lamaseweralo.
-