-
Machitidwe 19:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kunena zoona, gulu lonselo linali litasokonezeka, ena ankafuula zina, ena zina. Moti ambiri sankadziwa nʼkomwe kuti nʼchifukwa chiyani asonkhana kumeneko.
-