-
Machitidwe 19:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Pamapeto pake, woyangʼanira mzinda atauza gulu la anthulo kuti likhale chete anati: “Anthu inu a mu Efeso, alipo kodi munthu amene sadziwa kuti mzinda wa Aefeso ndi umene umayangʼanira kachisi wa Atemi wamkulu ndi chifaniziro chimene chinagwa kuchokera kumwamba?
-