Machitidwe 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero Paulo anapitanso mʼchipinda chamʼmwamba chija ndipo anatenga mkate nʼkuyamba kudya.* Anakambirana nawo kwa nthawi yaitali mpaka mʼbandakucha ndipo kenako ananyamuka nʼkumapita.
11 Atatero Paulo anapitanso mʼchipinda chamʼmwamba chija ndipo anatenga mkate nʼkuyamba kudya.* Anakambirana nawo kwa nthawi yaitali mpaka mʼbandakucha ndipo kenako ananyamuka nʼkumapita.