Machitidwe 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma tsopano ndikukusiyani kuti mutetezedwe ndi Mulungu ndiponso mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyera onse.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:32 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 22
32 Koma tsopano ndikukusiyani kuti mutetezedwe ndi Mulungu ndiponso mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyera onse.+