Machitidwe 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tinafufuza ophunzira ndipo titawapeza tinakhala nawo masiku 7. Koma mouziridwa ndi mzimu, iwo anauza Paulo mobwerezabwereza kuti asayerekeze kupita ku Yerusalemu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 175
4 Tinafufuza ophunzira ndipo titawapeza tinakhala nawo masiku 7. Koma mouziridwa ndi mzimu, iwo anauza Paulo mobwerezabwereza kuti asayerekeze kupita ku Yerusalemu.+