-
Machitidwe 21:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Masiku athu okhala kumeneko atatha, tinanyamuka kuti tipitirize ulendo wathu. Abale onse komanso azimayi ndi ana, anatiperekeza mpaka kunja kwa mzindawo. Kumeneko tinagwada mʼmbali mwa nyanja nʼkupemphera.
-