-
Machitidwe 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho tinanyamuka ku Turo pangalawa ndipo tinafika ku Tolemayi. Kumeneko tinapereka moni kwa abale nʼkukhala nawo tsiku limodzi.
-