Machitidwe 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lotsatira tinanyamuka nʼkukafika ku Kaisareya ndipo tinapita kunyumba kwa mlaliki wina dzina lake Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7+ a mbiri yabwino aja, ndipo tinakhala naye. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:8 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 176-177 Nsanja ya Olonda,7/15/1999, tsa. 259/1/1992, tsa. 17
8 Tsiku lotsatira tinanyamuka nʼkukafika ku Kaisareya ndipo tinapita kunyumba kwa mlaliki wina dzina lake Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7+ a mbiri yabwino aja, ndipo tinakhala naye.