Machitidwe 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Paulo anayankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukulira ndiponso kufuna kundifooketsa? Inetu ndine wokonzeka osati kumangidwa kokha, komanso kukafa ku Yerusalemu chifukwa cha dzina la Ambuye Yesu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:13 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 177-178 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 32
13 Koma Paulo anayankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukulira ndiponso kufuna kundifooketsa? Inetu ndine wokonzeka osati kumangidwa kokha, komanso kukafa ku Yerusalemu chifukwa cha dzina la Ambuye Yesu.”+