Machitidwe 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Titalephera kumusintha maganizo, tinasiya kumuletsa* nʼkunena kuti: “Chifuniro cha Yehova* chichitike.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:14 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 178
14 Titalephera kumusintha maganizo, tinasiya kumuletsa* nʼkunena kuti: “Chifuniro cha Yehova* chichitike.”