-
Machitidwe 21:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma ophunzira ena a ku Kaisareya ananyamuka nafe kuti atiperekeze kunyumba kwa Mnaso wa ku Kupuro, kuti tikafikire kumeneko. Munthu ameneyu anali mmodzi wa ophunzira oyambirira.
-