Machitidwe 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho tsiku lotsatira, Paulo anatenga amunawo nʼkukachita nawo mwambo wa kudziyeretsa.+ Kenako analowa mʼkachisi, kukanena pamene masiku awo a mwambo wa kudziyeretsa adzathere ndiponso pamene adzapereke nsembe ya aliyense.
26 Choncho tsiku lotsatira, Paulo anatenga amunawo nʼkukachita nawo mwambo wa kudziyeretsa.+ Kenako analowa mʼkachisi, kukanena pamene masiku awo a mwambo wa kudziyeretsa adzathere ndiponso pamene adzapereke nsembe ya aliyense.