-
Machitidwe 21:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Masiku 7 atatsala pangʼono kutha, Ayuda ochokera ku Asia anaona Paulo ali mʼkachisi. Choncho anachititsa kuti pagulu lonse la anthu payambike chisokonezo ndipo anamugwira.
-