-
Machitidwe 21:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Koma atatsala pangʼono kulowa naye kumpanda wa asilikali, Paulo anapempha mkulu wa asilikali kuti: “Kodi mungandilole kuti ndilankhule nanu pangʼono?” Iye anati: “Kani umalankhula Chigiriki?
-