Machitidwe 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Paulo anayankha kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, ndiloleni ndilankhule kwa anthuwa.”
39 Paulo anayankha kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, ndiloleni ndilankhule kwa anthuwa.”