Machitidwe 21:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe nʼkukwezera anthuwo dzanja. Onse atakhala chete, analankhula nawo mʼChiheberi+ kuti:
40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe nʼkukwezera anthuwo dzanja. Onse atakhala chete, analankhula nawo mʼChiheberi+ kuti: