Machitidwe 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno iye anati: ‘Mulungu wa makolo athu wakusankha kuti udziwe chifuniro chake, uone wolungamayo+ ndiponso umve mawu apakamwa pake.
14 Ndiyeno iye anati: ‘Mulungu wa makolo athu wakusankha kuti udziwe chifuniro chake, uone wolungamayo+ ndiponso umve mawu apakamwa pake.