Machitidwe 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa udzakhala mboni yake kwa anthu onse pa zinthu zimene waona komanso kumva.+