Machitidwe 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 mkulu wa asilikali analamula kuti alowe naye kumpanda wa asilikali. Iye anati ayenera kumufunsa mafunso kwinaku akumʼkwapula kuti adziwe chimene chachititsa kuti anthu azimukuwiza* choncho. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:24 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, ptsa. 21-226/15/1990, tsa. 23
24 mkulu wa asilikali analamula kuti alowe naye kumpanda wa asilikali. Iye anati ayenera kumufunsa mafunso kwinaku akumʼkwapula kuti adziwe chimene chachititsa kuti anthu azimukuwiza* choncho.