Machitidwe 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Paulo ataona kuti ena a iwo anali Asaduki ndipo ena anali Afarisi, anafuula mʼkhotimo kuti: “Anthu inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 187-188 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, tsa. 31
6 Paulo ataona kuti ena a iwo anali Asaduki ndipo ena anali Afarisi, anafuula mʼkhotimo kuti: “Anthu inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka.”