Machitidwe 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho panali chiphokoso, ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira nʼkuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza chimene munthuyu walakwa. Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye+ . . .” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 188
9 Choncho panali chiphokoso, ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira nʼkuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza chimene munthuyu walakwa. Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye+ . . .”