-
Machitidwe 23:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Choncho analamula asilikali kuti apite akamuchotse pagululo nʼkubwera naye kumpanda wa asilikali.
-