Machitidwe 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho bwanamkubwayo anawerenga kalatayo ndipo anafunsa chigawo chimene Paulo ankachokera. Anamva kuti ankachokera ku Kilikiya.+
34 Choncho bwanamkubwayo anawerenga kalatayo ndipo anafunsa chigawo chimene Paulo ankachokera. Anamva kuti ankachokera ku Kilikiya.+