Machitidwe 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinkachita zimenezi, anandipeza mʼkachisi nditadziyeretsa motsatira mwambo.+ Panalibe gulu la anthu kapena phokoso, koma panali Ayuda ena ochokera mʼchigawo cha Asia.
18 Pamene ndinkachita zimenezi, anandipeza mʼkachisi nditadziyeretsa motsatira mwambo.+ Panalibe gulu la anthu kapena phokoso, koma panali Ayuda ena ochokera mʼchigawo cha Asia.