Machitidwe 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Popeza Felike ankadziwa bwino nkhani yokhudza Njira imeneyi,+ anaimitsa mlanduwo nʼkunena kuti: “Ndidzagamula mlandu wanuwu akadzafika Lusiya mkulu wa asilikali.”
22 Popeza Felike ankadziwa bwino nkhani yokhudza Njira imeneyi,+ anaimitsa mlanduwo nʼkunena kuti: “Ndidzagamula mlandu wanuwu akadzafika Lusiya mkulu wa asilikali.”