-
Machitidwe 24:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iye analamula mtsogoleri wa asilikali kuti amusunge mʼndende, koma amupatseko ufulu ndipo azilola anthu a mtundu wake kudzamuthandiza.
-