Machitidwe 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita masiku angapo, Felike anafika pamodzi ndi mkazi wake Durusila, amene anali Myuda. Ndiyeno Felike anaitanitsa Paulo nʼkumamvetsera pamene ankafotokoza za kukhulupirira Khristu Yesu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:24 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 194-195
24 Patapita masiku angapo, Felike anafika pamodzi ndi mkazi wake Durusila, amene anali Myuda. Ndiyeno Felike anaitanitsa Paulo nʼkumamvetsera pamene ankafotokoza za kukhulupirira Khristu Yesu.+