Machitidwe 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti awakomere mtima nʼkuitanitsa Paulo kuti abwere ku Yerusalemu. Koma anakonza zoti amudikirire panjira nʼkumupha.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 196
3 kuti awakomere mtima nʼkuitanitsa Paulo kuti abwere ku Yerusalemu. Koma anakonza zoti amudikirire panjira nʼkumupha.+