Machitidwe 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Paulo anapempha kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka.+ Choncho ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”
21 Koma Paulo anapempha kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka.+ Choncho ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”