Machitidwe 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera kuphedwa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka, ndinaganiza zomutumiza.
25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera kuphedwa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka, ndinaganiza zomutumiza.