Machitidwe 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 amene akundidziwa kuyambira kale. Atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi+ wa mʼgulu limene limalambira mokhwimitsa zinthu kwambiri.+
5 amene akundidziwa kuyambira kale. Atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi+ wa mʼgulu limene limalambira mokhwimitsa zinthu kwambiri.+