Machitidwe 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli ndipo akumuchitira Mulunguyo utumiki wopatulika mosalekeza masana ndi usiku. Choncho Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:7 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 199
7 Mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli ndipo akumuchitira Mulunguyo utumiki wopatulika mosalekeza masana ndi usiku. Choncho Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+