Machitidwe 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo izi ndi zimene ndinachitadi ku Yerusalemu. Ndinkatsekera mʼndende oyera ambiri+ nditapatsidwa mphamvu ndi ansembe aakulu.+ Akaweruzidwa kuti aphedwe, ine ndinkavomereza. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:10 Nsanja ya Olonda,6/15/1999, tsa. 30
10 Ndipo izi ndi zimene ndinachitadi ku Yerusalemu. Ndinkatsekera mʼndende oyera ambiri+ nditapatsidwa mphamvu ndi ansembe aakulu.+ Akaweruzidwa kuti aphedwe, ine ndinkavomereza.