Machitidwe 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuyambira kwa anthu a ku Damasiko,+ kenako a ku Yerusalemu+ ndipo kenako mʼdziko lonse la Yudeya ndi anthu a mitundu ina, ndinafikitsa uthenga wakuti alape nʼkuyamba kulambira Mulungu pochita zinthu zosonyeza kulapa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 200-201
20 Kuyambira kwa anthu a ku Damasiko,+ kenako a ku Yerusalemu+ ndipo kenako mʼdziko lonse la Yudeya ndi anthu a mitundu ina, ndinafikitsa uthenga wakuti alape nʼkuyamba kulambira Mulungu pochita zinthu zosonyeza kulapa.+