Machitidwe 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe, popeza ndinaona Mulungu akundithandiza, ndikuchitirabe umboni kwa anthu otchuka ndiponso anthu wamba mpaka lero. Sindikunena chilichonse, koma zokhazo zimene aneneri ndi Mose ananena kuti zichitika.+
22 Komabe, popeza ndinaona Mulungu akundithandiza, ndikuchitirabe umboni kwa anthu otchuka ndiponso anthu wamba mpaka lero. Sindikunena chilichonse, koma zokhazo zimene aneneri ndi Mose ananena kuti zichitika.+