Machitidwe 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ku Adiramutiyo tinakwera ngalawa imene inali itatsala pangʼono kunyamuka ulendo wopita kumadoko amʼmbali mwa nyanja mʼchigawo cha Asia. Kenako tinanyamuka limodzi ndi Arisitako,+ yemwe anali wa ku Makedoniya ku Tesalonika. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 204 Nsanja ya Olonda,9/15/1997, ptsa. 30-31
2 Ku Adiramutiyo tinakwera ngalawa imene inali itatsala pangʼono kunyamuka ulendo wopita kumadoko amʼmbali mwa nyanja mʼchigawo cha Asia. Kenako tinanyamuka limodzi ndi Arisitako,+ yemwe anali wa ku Makedoniya ku Tesalonika.