-
Machitidwe 27:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Tsiku lotsatira tinafika ku Sidoni, ndipo Yuliyo anakomera mtima Paulo moti anamulola kupita kwa anzake kuti akamusamalire.
-