-
Machitidwe 27:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho tinayenda pangʼonopangʼono kwa masiku angapo ndipo tinafika ku Kinido movutikira. Chifukwa cha mphepo yomwe inkawomba kuchokera kutsogolo kwathu, tinadzera ku Salimone kuti chilumba cha Kerete chizititeteza ku mphepoyo.
-