Machitidwe 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pasanapite nthawi, mphepo yamkuntho yotchedwa Yulakilo* inayamba kuwomba ngalawayo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:14 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 207 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 24