-
Machitidwe 27:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma popeza mphepo yamkuntho inkatiwomba ndiponso kutikankha mwamphamvu, tsiku lotsatira anthu anayamba kutaya katundu kuti ngalawa ipepukidwe.
-